Ukhale Wanga
Ukhale Wanga

Ukhale Wanga Lyrics Meanings
by Onee Official

Sep 8, 2021
18
Ukhale Wanga Music Video

Ukhale Wanga Lyrics

Soundshow music
Za iwe

Nkani ndikufuna kupanga zaiwe
Ndimafuna utakhala waine
All i need is your loving
Be my queen come on my way baby
Be my queen come on my way aah
Umandipatsa nkhani osanama baby ndiwe one
Bwela nkupase plan
Poti watenga kale yanga mbali
Ndi mu m'dima ndikufuna nyali
Nde ndiweyo ndiweyo

Baby ukhale wanga
Ukhale wanga
Malawian beautiful
Baby ukhale wanga
Ukhale wanga
Ukhale wanga

Hey girl ndayamba kukupanga escort mpaka nthawi
Sukundiuza zomwe zilimu ntima mwako
Tell what's in mind
Ndikufunisitsa undipase mwayi nkhale nawe
Uwugwilisitse ntima wanga usautaye
And i promise you i will be there for you singakuthawe
baby

Baby ukhale wanga
Ukhale wanga
Malawian beautiful
Baby ukhale wanga
Ukhale wanga
Ukhale wanga

Ukhale wanga
Ukhale wanga
Ukhale wanga
Ukhale wanga
Baby ukhale wanga
Ukhale wanga

Writer(s): Paul Batson
Copyright(s): Lyrics Ā© DistroKid
Lyrics Licensed & Provided by LyricFind

Ukhale Wanga Meanings

This is a love song, the title of the song UKHALE WANGA means BE MINE

End of content

That's all we got for #

What Does Ukhale Wanga Mean?

Attach an image to this thought

Drag image here or click to upload image

Latest Blog Posts
Lyrics Discussions
Hot Tracks
Up
by Cardi B

0

146

0

3K
Recent Blog Posts